Mfundo Zachidule—Togo
- 9,515,000—Chiwerengero cha anthu
- 24,471—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 392—Mipingo
- Pa anthu 398 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Anadzipereka ndi Mtima Wonse Kumadzulo kwa Africa
Kodi n’chiyani chinalimbikitsa Akhristu ena ku Ulaya kuti asamukire kumadzulo kwa Africa, nanga zinthu zikuwayendera bwanji kumeneko?