Mfundo Zachidule—Slovakia
- 5,427,000—Chiwerengero cha anthu
- 11,333—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 135—Mipingo
- Pa anthu 485 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
Dera la Štrbské Pleso ku Slovakia—Akugawira kapepala kakuti Kodi Dziko Lapansili Lili M’manja mwa Ndani?