Mfundo Zachidule—Netherlands
- 17,951,000—Chiwerengero cha anthu
- 29,618—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 340—Mipingo
- Pa anthu 610 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
NSANJA YA OLONDA (YOPHUNZIRA)
Timasangalala Kutumikira Yehova Kwina Kulikonse
Werengani kuti mudziwe zimene banja lina la ku Netherlands lachita kuti lizikhulupirira Yehova ndi mtima wonse ngakhale kuti utumiki wawo unkasinthasintha komanso ankakumana ndi mavuto.