Mfundo Zachidule—Guinea-Bissau
- 2,197,000—Chiwerengero cha anthu
- 215—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 4—Mipingo
- Pa anthu 10,665 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
Kupul, Guinea-Bissau—Akukambirana mfundo za m’Baibulo ndi mlimi m’chinenero cha Chipwitikizi cha Chikiliyo