Mfundo Zachidule—Cape Verde
- 604,000—Chiwerengero cha anthu
- 2,280—Chiwerengero cha Mboni za Yehova
- 35—Mipingo
- Pa anthu 270 alionse pali wa Mboni za Yehova m’modzi
Mzinda wa Mindelo, m’dziko la Cape Verde—Akugawira kabuku kakuti, Uthenga Wabwino Wochokera kwa Mulungu