Tipezeni
Timasangalala kuthandiza anthu amene akufunitsitsa kuphunzira Baibulo komanso amene akufuna kudziwa zomwe timachita padziko lonse. Sankhani chimodzi mwa zinthu zomwe zili m’munsizi kuti mukumane ndi a Mboni za Yehova m’dera lanu.
Onani tsiku limene Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu wotsatira udzachitike
Pezani kumene kukuchitikira msonkhano waukulu wa Mboni za Yehova
Tiimbireni kapena tilembereni pogwiritsa ntchito zinthu zomwe zili m’munsizi
Mali
Association Les Témoins de Jéhovah du Sénégal
BP 29896
12000 DAKAR
SENEGAL
+221 33-820-80-00
Nthawi Yogwira Ntchito
Lolemba mpaka Lachisanu
8:00 a.m. mpaka 12:30 p.m. komanso 1:45 p.m. mpaka 5:15 p.m. (Mali / GMT)