Misonkhano Ikuluikulu Yapachaka ya Mboni za Yehova
Chaka chilichonse a Mboni za Yehova amakhala ndi misonkhano ya masiku atatu. Pa misonkhanoyi pamakambidwa nkhani komanso pamaonetsedwa mavidiyo omwe amafotokoza zimene tingaphunzire kuchokera m’Baibulo. Fufuzani kumene misonkhanoyi imachitikira m’dera lanu.