Kuona Malo ku Beteli
Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.
Solomon Islands
Lot 3142
Panatina Village
HONIARA
SOLOMON ISLANDS
+677 22241
Kuona Malo
Lolemba mpaka Lachisanu
8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.
Nthawi yonse: Ola limodzi
Zimene Timachita
Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’zinenero 6.