Kuona Malo ku Beteli
Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.
Philippines
186 Roosevelt Ave
San Francisco del Monte
1105 QUEZON CITY
PHILIPPINES
+63 2-372-3745
+63 2-411-6090
Kuona Malo
Lolemba mpaka Lachisanu
8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.
Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu
Zimene Timachita
Timamasulira magazini a Nsanja ya Olonda m’zinenero 7 zikuluzikulu za ku Philippines. Timajambula mavidiyo ndi zinthu zina zomvetsera m’zinenero 8. Timatumiza mabuku kumipingo yoposa 3,000.