Kuona Malo ku Beteli
Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.
Nigeria
Km 51, Benin-Auchi Road
IGIEDUMA 301110
EDO STATE
NIGERIA
+234 7080-662-020
+234 8039-003-790
Kuona Malo
Lolemba mpaka Lachisanu
8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.
Nthawi yonse: Maola awiri
Zimene Timachita
Chaka chilichonse, timasindikiza magazini a Nsanja ya Olonda ndi Galamukani! okwana 41 miliyoni m’zinenero 9. Timatumiza mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo ku Nigeria ndi kumayiko ena asanu a kumadzulo kwa Africa