Kuona Malo ku Beteli
Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.
Ecuador
Sociedad de Estudiantes de la Biblia - Testigos de Jehová
Kilometer 23,5 via a la Costa (mamita 600 musanapeze maofesi olandirira misonkho)
GUAYAQUIL
ECUADOR
+593 4-371-2720
Kuona Malo
Lolemba mpaka Lachisanu
8:30 a.m. mpaka 10:30 a.m. ndi 1:30 p.m. mpaka 3:30 p.m.
Nthawi yonse: Ola limodzi ndi hafu
Zimene Timachita
Timayang’anira mipingo yoposa 900. Timamasulira mabuku ofotokoza nkhani za m’Baibulo m’Chikichuwa ndi zinenero zina zofanana nacho, komanso chinenero chamanja cha ku Ecuador ndi Chishuwa.