Kuona Malo ku Beteli
Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.
Chile
Ave Concha y Toro 3456
PUENTE ALTO
CHILE
+56 2-428-2600
+56 2-428-2609 (Fax)
Kuona Malo
Lolemba mpaka Lachisanu
8:30 a.m., 9:30 a.m., 10:30 a.m., 1:30 p.m., 2:30 p.m., 3:30 p.m.
Nthawi yonse: Ola limodzi
Zimene Timachita
Timayang’anira ntchito yophunzitsa anthu Baibulo imene Mboni za Yehova zikugwira ku Chile. Timatumiza mabuku kumipingo yoposa 800.