Kuona Malo ku Beteli
Tikukuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi omwenso amadziwika kuti Beteli. Ku maofesi athu ena kulinso malo achionetsero omwe mukhoza kuona nokha popanda wokutsogolerani.
Albania
Autostrada Tiranë – Durrës, Km 1
Mëzez
TIRANË
ALBANIA
+355 42-407-255
Onani Mapu
Kuona Malo
Lolemba mpaka Lachisanu
8:00 a.m. mpaka 11:00 a.m. ndi 1:00 p.m. mpaka 4:00 p.m.
Nthawi yonse: Ola limodzi
Zimene Timachita
Timamasulira mabuku ofotokoza Baibulo m’Chiabeniya ndiponso m’chinenero chamanja cha ku Albania. Timatumiza mabuku a m’zinenero zosiyanasiyana m’mipingo ya ku Albania ndi ku Kosovo.