Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu

Mmene Mungapezere Malemba M’Baibulo Lanu

Mndandanda wa Mabuku a M’Baibulo a

Buku

Amene Analemba

Kumalizidwa

Genesis

Mose

1513 B.C.E.

Ekisodo

Mose

1512 B.C.E.

Levitiko

Mose

1512 B.C.E.

Numeri

Mose

1473 B.C.E.

Deuteronomo

Mose

1473 B.C.E.

Yoswa

Yoswa

c. 1450 B.C.E.

Oweruza

Samueli

c. 1100 B.C.E.

Rute

Samueli

c. 1090 B.C.E.

1 Samueli

Samueli; Gadi; Natani

c. 1078 B.C.E.

2 Samueli

Gadi; Natani

c. 1040 B.C.E.

1 Mafumu

Yeremiya

580 B.C.E.

2 Mafumu

Yeremiya

580 B.C.E.

1 Mbiri

Ezara

c. 460 B.C.E.

2 Mbiri

Ezara

c. 460 B.C.E.

Ezara

Ezara

c. 460 B.C.E.

Nehemiya

Nehemiya

a. 443 B.C.E.

Esitere

Moredikayi

c. 475 B.C.E.

Yobu

Mose

c. 1473 B.C.E.

Masalimo

Davide ndi ena

c. 460 B.C.E.

Miyambo

Solomo; Aguri; Lemuele

c. 717 B.C.E.

Mlaliki

Solomo

b. 1000 B.C.E.

Nyimbo ya Solomo

Solomo

c. 1020 B.C.E.

Yesaya

Yesaya

a. 732 B.C.E.

Yeremiya

Yeremiya

580 B.C.E.

Maliro

Yeremiya

607 B.C.E.

Ezekieli

Ezekieli

c. 591 B.C.E.

Danieli

Danieli

c. 536 B.C.E.

Hoseya

Hoseya

a. 745 B.C.E.

Yoweli

Yoweli

c. 820 B.C.E. (?)

Amosi

Amosi

c. 804 B.C.E.

Obadiya

Obadiya

c. 607 B.C.E.

Yona

Yona

c. 844 B.C.E.

Mika

Mika

b. 717 B.C.E.

Nahumu

Nahumu

b. 632 B.C.E.

Habakuku

Habakuku

c. 628 B.C.E. (?)

Zefaniya

Zefaniya

b. 648 B.C.E.

Hagai

Hagai

520 B.C.E.

Zekariya

Zekariya

518 B.C.E.

Malaki

Malaki

a. 443 B.C.E.

Mateyu

Mateyu

c. 41 C.E.

Maliko

Maliko

c. 60-​65 C.E.

Luka

Luka

c. 56-​58 C.E.

Yohane

Mtumwi Yohane

c. 98 C.E.

Machitidwe

Luka

c. 61 C.E.

Aroma

Paulo

c. 56 C.E.

1 Akorinto

Paulo

c. 55 C.E.

2 Akorinto

Paulo

c. 55 C.E.

Agalatiya

Paulo

c. 50-​52 C.E.

Aefeso

Paulo

c. 60-​61 C.E.

Afilipi

Paulo

c. 60-​61 C.E.

Akolose

Paulo

c. 60-​61 C.E.

1 Atesalonika

Paulo

c. 50 C.E.

2 Atesalonika

Paulo

c. 51 C.E.

1 Timoteyo

Paulo

c. 61-​64 C.E.

2 Timoteyo

Paulo

c. 65 C.E.

Tito

Paulo

c. 61-​64 C.E.

Filimoni

Paulo

c. 60-​61 C.E.

Aheberi

Paulo

c. 61 C.E.

Yakobo

Yakobo (mchimwene wa Yesu)

b. 62 C.E.

1 Petulo

Petulo

c. 62-​64 C.E.

2 Petulo

Petulo

c. 64 C.E.

1 Yohane

Mtumwi Yohane

c. 98 C.E.

2 Yohane

Mtumwi Yohane

c. 98 C.E.

3 Yohane

Mtumwi Yohane

c. 98 C.E.

Yuda

Yuda (mchimwene wa Yesu)

c. 65 C.E.

Chivumbulutso

Mtumwi Yohane

c. 96 C.E.

Dziwani izi: Mabuku ena sakudziwika bwinobwino amene analemba komanso nthawi imene anamalizidwa. Madeti ambiri ndi ongoyerekezera ndipo pomwe pali a. zikutanthauza “chitadutsa chaka cha,” b. kutanthauza “chisanafike chaka cha,” ndiponso c. kutanthauza “cha m’ma.”

a Mndandandawu ukusonyeza mabuku 66 a m’Baibulo ndipo aikidwa motsatira mmene aliri m’ma Baibulo ambiri. Mndandandawu unapangidwa mu 300 B.C.E.