Yehova Amatitsogolera Panjira Yamtendere—Mbali Yoyamba
Kuganizira nkhani za m’Baibulo za atumiki akale okhulupirika kumatithandiza kuti tizikhulupirira kwambiri zoti Yehova amateteza anthu omwe amamudalira masiku ano.