NSANJA YA OLONDA October 2014 | Kodi Ufumu wa Mulungu Udzakuchitirani Chiyani?
Yankho la funsoli lagona pa mmene Yesu, Atate wake komanso anthu okhulupirika amaonera Ufumuwu.
NKHANI YAPACHIKUTO
N’chifukwa Chiyani Muyenera Kudziwa Zambiri Zokhudza Ufumu wa Mulungu?
N’chifukwa chiyani a Mboni za Yehova amalalikira za Ufumu wa Mulungu pamene zipembedzo zina zachikhristu sizikonda kulalikira za Ufumuwu?
NKHANI YAPACHIKUTO
Yesu Amaona Kuti Ufumu wa Mulungu Ndi Wofunika Kwambiri
Yesu ankakonda kuuza anthu zokhudza Ufumu wa Mulungu kuposa nkhani iliyonse chifukwa ankadziwa kuti Ufumuwu ndi wofunika kwambiri.
NKHANI YAPACHIKUTO
Kodi Ufumu wa Mulungu Udzakuchitirani Chiyani?
Zimene udzakuchitireni zikudalira zimene mukuchita panopa.
KUCHEZA NDI MUNTHU WINA
Kodi Ufumu wa Mulungu Unayamba Liti Kulamulira? (Gawo 1)
Ngati mukudziwa yankho lake, kodi mungamufotokozere munthu wina bwinobwino kuchokera m’Baibulo?
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Ndinali Munthu Wodzikonda Kwambiri
Christof Bauer ankawerenga Baibulo ali m’boti pakati pa nyanja ya Atlantic. Kodi anaphunzira zotani?
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
Kodi Ufumu wa Mulungu udzachita chiyani chimene maboma a anthu sangakwanitse kuchita?
Zina zimene zili pawebusaiti
Kodi Mulungu Angayankhe Mapemphero Anga?
Kuti Mulungu ayankhe mapemphero anu zimadalira kwambiri pa zimene inuyo mumachita.