NSANJA YA OLONDA August 2014 | Kodi Mulungu Amakuonani Kuti Ndinu Wofunika?
Kodi n’chiyani chimasonyeza kuti Mulungu amatiganizira?
NKHANI YAPACHIKUTO
Kodi Mulungu Amakuganizirani?
Kodi n’zoona kuti Mulungu Wamphamvuyonse amakuganizirani inuyo?
NKHANI YAPACHIKUTO
Mulungu Amaona Zomwe Zikuchitika pa Moyo Wanu
N’chifukwa chiyani amatchedwa ‘Mulungu amene amaona chilichonse’?
NKHANI YAPACHIKUTO
Mulungu Amakumvetsani
Mulungu akamafufuza mtima wanu, samangoona zomwe mumalakwitsa. WEB:OnSiteAdTitleMulungu Amakumvetsani
NKHANI YAPACHIKUTO
Mulungu Angakulimbikitseni ndi Kukuthandizani
Kodi mungatani ngati mukuona kuti mavuto anu ndi ochepa kwambiri mukayerekezera ndi mavuto adzaoneni amene anthu ena akukumana nawo?
NKHANI YAPACHIKUTO
Mulungu Akufuna Kuti Mukhale Naye pa Ubwenzi
Kodi mungatani ngati mumakhulupirira kuti kuli Mulungu koma mukuona kuti simuli naye pa ubwenzi?
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
Ndinkamenya Nkhondo Yangayanga Yolimbana Ndi Kupanda Chilungamo Komanso Chiwawa
Antoine Touma anali katswiri wa Kung Fu, koma lemba la 1 Timoteyo 4:8 linamuthandiza kuti asinthe.
TSANZIRANI CHIKHULUPIRIRO CHAWO
“Tamverani Maloto Amene Ine Ndinalota”
Mabanja ambiri omwe muli makolo ndi ana opeza angaphunzire zambiri pa zimene zinkachitika m’banja lomwe Yosefe anakulira.
ZIMENE OWERENGA AMAFUNSA
Kodi Ndani Analenga Mulungu?
Kodi n’zosamveka kunena kuti Mulungu alibe chiyambi?
Kuyankha Mafunso a M’Baibulo
Kodi n’zoona kuti pali zipembedzo zina zimene sizikondweretsa Mulungu?
Zina zimene zili pawebusaiti
Kodi Mulungu Ndi Mphamvu Yosaoneka?
Baibulo limanena kuti Mulungu analenga zinthu zonse. Koma kodi iye amatiwerengera?