Tsamba 32
Tsamba 32
▪ Dziwani njira yabwino kwambiri yothetsera mavuto onse amene tikukumana nawo masiku ano. Onani tsamba 5.
▪ Anthu amene anapulumuka pamene mwana wasukulu anapha anthu pasukulu ina ku Winnenden, m’dziko la Germany, akufotokoza chimene chikuwathandiza kupirira zoopsazi. Onani tsamba 9.
▪ Kodi ndi Mfumu Herode uti amene ankafuna kupha Yesu ali wakhanda? Onani tsamba 13.
▪ Kodi mukudziwapo chiyani pachikondwerero chimene chimachitika ku Asia pakapita mwezi umodzi m’chaka chatsopano? Onani tsamba 20.
▪ Dziwani nkhani yokhudza nyimbo za m’nthawi ya Baibulo, pophunzira moyo wa Mfumu Davide. Onani tsamba 26.
▪ Panthawi imene Yesu anali modyeramo ziweto, kodi panabweradi mafumu atatu, kapena kuti anzeru a kum’mawa, kudzalambira? Onani tsamba 31.
[Mawu a Chithunzi patsamba 32]
Starving children: WHO/OXFAM