Tsamba 32
Tsamba 32
▪ Kodi n’chiyani chingakuthandizeni kukhala ndi mtendere wa mumtima ngakhale muli pa umphawi, mukudwala kapena mukuona kuti mukhoza kumwalira?
▪ Kodi kupemphera m’dzina la Yesu n’kofunika pa zifukwa zitatu ziti?
▪ N’chifukwa chiyani lilime tingaliyerekezere ndi moto?
▪ N’chifukwa chiyani Mulungu amalola kuti tizivutika?
▪ Kodi ndi mavuto ena ati amene azimayi omwe ali pantchito amakumana nawo kawirikawiri?