Mlozera Nkhani wa Magazini a Nsanja ya Olonda a 2015
Wosonyeza deti la magazini imene muli nkhaniyo
BAIBULO
BAIBULO LIMASINTHA ANTHU
MAFUNSO OCHOKERA KWA OWERENGA
Abale ndi alongo amene amavutika akamva fungo la perefyumu, 2/15
Kodi mlongo azivala chinachake kumutu pochititsa phunziro ndi m’bale amene ndi wofalitsa? 2/15
Kodi mzinda wakale wa Yeriko unagonjetsedwa m’kanthawi kochepa? 11/15
N’chifukwa chiyani safotokozanso kuti zinthu zosiyanasiyana zimaphiphiritsira zinazake? 3/15
MBIRI YA MOYO WATHU
Chikondi Changa cha Poyamba Chandithandiza Kupirira (A. Morris III), 5/15
Chuma Chomwe Chakhala ku Banja Lathu kwa Mibadwo 7 (K. Williams), 6/1
Ndadalitsidwa “M’nthawi Yabwino ndi M’nthawi Yovuta” (T. R. Nsomba), 4/15
Ndili pa Mtendere ndi Mulungu Komanso Amayi Anga (M. Kumagai), 12/15
Ndinapeza Chinthu Chamtengo Wapatali Kuposa Kukhala Wotchuka (M. H. Godenzi), 9/1
Tinapeza Ntchito Yabwino Kwambiri (D. ndi G. Cartwright), 3/15
MBONI ZA YEHOVA
MOYO NDI MAKHALIDWE ACHIKHRISTU
NKHANI ZOPHUNZIRA
Kodi Chikumbumtima Chanu Chimakuthandizani Kusankha Zochita Mwanzeru? 9/15
Kodi ‘Mumakonda Anzanu Ngati Mmene Mumadzikondera Nokha’? 11/15
Lolani Kuti Yehova Alimbitse Ndiponso Kuteteza Banja Lanu, 1/15
Muziphunzitsa Ana Anu Aang’ono Kuti Azitumikira Yehova, 11/15
Muziphunzitsa Ana Anu Achinyamata Kuti Azitumikira Yehova, 11/15
N’chifukwa Chiyani Timachita Mwambo Wokumbukira Imfa ya Yesu? 1/15
Tizisankha Mwanzeru Anthu Ocheza Nawo M’masiku Otsiriza Ano, 8/15
Zimene Zachitika M’zaka 100 Zimene Ufumu Wakhala Ukulamulira, 11/15
Zinthu Zimene Zinathandiza Kuti Anthu Aphunzire za Yehova, 2/15
NKHANI ZOSIYANASIYANA
Kodi Ayuda Omwe Anabwera pa Pentekosite mu 33 C.E. Anachokeradi ‘mu Mtundu Uliwonse’? 12/1
Kodi Tinalengedwa Kuti Tizingokhalako kwa Nthawi Yochepa? 8/1
“Mwana Wanga Wokondedwa ndi Wokhulupirika mwa Ambuye” (Timoteyo), 11/1
N’chifukwa Chiyani Anthu a ku Melita Ankaganiza Kuti Paulo Ndi Chigawenga? 10/1
N’chifukwa Chiyani Yosefe Anayamba Wameta Asanakaonane ndi Farao? 11/1
Zimene Ofukula Zinthu Zakale Anapeza Zimagwirizana ndi Baibulo? 5/1
YEHOVA