Zimene Zili M’magaziniyi
Zipangizo zamakono zikhoza kusokoneza anthu pang’ono ndi pang’ono komanso m’njira yoti sangathe kuizindikira.
KODI ZIPANGIZO ZAMAKONO ZIMAKHUDZA BWANJI . . .
Ubwenzi Wanu ndi Anzanu?
Ana Anu?
Banja Lanu?
Mmene Mumaganizira?