Mlozera Nkhani wa Magazini a Galamukani! a 2012
CHIPEMBEDZO
Baibulo Ndi Buku la Maulosi Olondola, 5/12, 6/12, 7/12, 8/12, 9/12, 10/12, 11/12, 12/12
Zimene Zingakuthandizeni Kulimvetsa Baibulo, 11/12
MAUNANSI A ANTHU
Kodi Mwana Wanu Amaopa Zoopsa Zomwe Zachitika? 10/12
Kufuna Kudzipha, 1/12
Kukhala Kholo Labwino, 10/12
Kuleza Mtima, 12/12
Kupsa Mtima, 3/12
Kuthandiza Mwana Yemwe Wachibale Wake Wamwalira, 7/12
Kuthandiza Odwala Matenda Oda Nkhawa, 3/12
Mabanja Omwe Ali Ndi Ana Opeza, 4/12
Makolo Omwe Akulera Okha Ana, 11/12
Malo Ochezera a pa Intaneti, 2/12
Muzikumbukira Kunena Kuti Zikomo Kwambiri, 7/12
MAYIKO NDI ANTHU
Batik—Nsalu Zokongola za ku Indonesia, 6/12
Caucasus Dera Lamapiri Komanso Zilankhulo Zosiyanasiyana, 12/12
Chiarabu Chinali Chinenero cha Anthu Ophunzira Kwambiri, 2/12
Chipatso Chokoma Kwambiri cha ku Armenia, 3/12
Chitoliro (Switzerland), 1/12
Kuteteza Zachilengedwe Kuti Zisatheretu (New Zealand), 4/12
Mpira wa EURO 2012 (Poland, Ukraine), 6/12
Mzinda wa Mapepala (Czech Republic), 2/12
Nkhondo ya ku Ain Jalut (Mongolia), 3/12
Nkhumba N’zofunika kwambiri (Papua New Guinea), 8/12
Nyumba Zachitetezo za ku Terezín (Czech Republic), 3/12
MBIRI YA MOYO WA ANTHU
Kukhala Bwenzi la Mulungu Ngakhale Utakalamba (O. Mattila), 1/12
Ndinkakonda Kuchita Zachiwawa (S. Garza), 8/12
Sanataye Nane Mtima (K. Lyons), 11/12
Tsopano Ndili Ndi Mtendere Wamumtima (E. Nahakbria), 6/12
MBONI ZA YEHOVA
Buku lachingelezi la Young People Ask, Volume I, 6/12
Galamukani! Yotsatira, 12/12
Msonkhano Wachigawo Wakuti, “Tetezani Mtima Wanu,” 5/12
Njira Zochizira Popanda Kuika Magazi (Russia), 9/12
Nyumba za Ufumu Zomwe Zamangidwa ku Malawi, 5/12
NYAMA NDI ZOMERA
Anyani a Chiyendayekha, 10/12
Bakha Wam’madzi, 11/12
Chipatso Chokoma Kwambiri cha ku Armenia, 3/12
Duwa Lalikulu Padziko Lonse, 8/12
Kodi Mumadya Bowa? 3/12
Kodi Munaonapo Ng’ombe Ngati Iyi? 12/12
Kodi N’zotheka Kuteteza Zachilengedwe Kuti Zisatheretu? 4/12
Koma Ndiye Chimphunotu! 5/12
Malo Osungira Nyama, 9/12
Mandimu, 9/12
Ndiwo Zokoma, 6/12
Nkhalango ya Tasmania, 4/12
Nkhanu Zam’nyanja, 7/12
Nkhumba, 8/12
Nsikidzi, 12/12
UMOYO NDI MANKHWALA
Akatswiri Akale a Zamankhwala, 9/12
Kunenepa Kwambiri, 10/12
Kusamalira Zakudya, 6/12
Matenda Oda Nkhawa, 3/12
Mtedza wa Betel, 2/12
Nyamakazi ya M’mafupa, 8/12
SAYANSI
Akatswiri Akale a Sayansi ya Zakuthambo, 4/12
Akatswiri Akale a Zamankhwala, 9/12
Akatswiri Akale Opanga Makina, 11/12
Chiarabu Chinali Chinenero Cha Anthu Ophunzira Kwambiri, 2/12
Kodi Zinangochitika Zokha? 1/12, 2/12, 3/12, 4/12, 5/12, 6/12, 7/12, 8/12, 9/12, 10/12, 11/12
Nyenyezi, 2/12
ZACHUMA NDI NTCHITO
Kodi Kuchita Zinthu Mwachilungamo N’kothandiza? 1/12
ZIMENE BAIBULO LIMANENA
“Choonadi Chidzakumasulani,” 5/12
Kodi Akufa Angathandize Amoyo? 6/12
Kodi Mulungu Amagwiritsa Ntchito Masoka Achilengedwe Kulanga Anthu? 12/12
Kodi Mumakhulupirira Nyenyezi? 10/12
Kodi Mumaona Kuti Chipembedzo N’chofunika? 9/12
Kodi Muyenera Kupita Pamalo Enaake Kuti Mukapemphere? 8/12
Kodi Ndani Angasinthe Zinthu Padzikoli? 7/12
Kodi Tizivomereza Khalidwe Logonana Amuna Kapena Akazi Okhaokha? 1/12
Kudzionetsera, 11/12
Kukhala pa Mtendere ndi Ena, 3/12
N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuyamikira Ena? 4/12
Tizitchula Zinthu Ziti Tikamapemphera Kwa Mulungu? 2/12
ZOTI BANJA LIKAMBIRANE
1/12, 2/12, 3/12, 4/12, 5/12, 6/12, 7/12, 8/12, 9/12, 10/12, 11/12, 12/12
ZOCHITIKA PA DZIKO
Chenjerani Ndi Zigawenga za pa Intaneti, 5/12
Kodi Zinthu Zidzasinthadi Padzikoli? 7/12
Ndani Angamve Kulira kwa Oponderezedwa? 5/12
Umbava wa pa Intaneti, 1/12
Zachiwawa, 8/12
ZOSIYANASIYANA
Dikishonale Yomwe Yatha Zaka 90 Ikulembedwa, 12/12
Gwiritsani Ntchito Maso Anu Mwanzeru, 2/12
Kubera Mayeso, 8/12
Kutha kwa Dziko, 9/12
Sitima ya Titanic, 4/12
Zimene Mungachite Kuti Zizikuyenderani ku Sukulu, 10/12
ZIMENE ACHINYAMATA AMADZIFUNSA
Kaya Ndinaneneranji Zimene Zija? 1/12
Kodi Mwamuna Weniweni Amakhala Wotani? 12/12
Kodi Ndimangocheza Naye Kapena Ndimamufuna? 6/12, 7/12
Kodi Ndimatengera Chitsanzo cha Ndani? 8/12
Kodi Ndingatani Kuti Ndizisangalala Ndikamawerenga Baibulo? 2/12
Kodi Ndingatani Ngati Ndapanikizika Maganizo? 11/12
Kodi Ndiziyembekezera Chiyani M’banja? 9/12, 10/12
Kodi Pali Vuto Lililonse Kukhala Wotchuka? 3/12
N’chifukwa Chiyani Makolo Anga Samandimvetsa? 5/12
N’chifukwa Chiyani Ndiyenera Kumapita ku Misonkhano ya Mpingo? 4/12