Lachisanu
“Tisaleke kuchita zabwino”—AGALATIYA 6:9
M’MAWA
-
9:20 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
9:30 Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero
-
9:40 NKHANI YA TCHEYAMANI: Tisafooke, Makamaka Panopa (Chivumbulutso 12:12)
-
10:15 NKHANI YOSIYIRANA: Pitirizani Kulalikira “Mwakhama”
-
Mwamwayi (Machitidwe 5:42; Mlaliki 11:6)
-
Kunyumba ndi Nyumba (Machitidwe 20:20)
-
M’malo Opezeka Anthu Ambiri (Machitidwe 17:17)
-
Muzithandiza Anthu Kuti Akhale Ophunzira a Yesu (Aroma 1:14-16; 1 Akorinto 3:6)
-
-
11:05 Nyimbo Na. 153 ndi Zilengezo
-
11:15 SEWERO LA MAWU OKHA: Yehova Amapulumutsa Anthu Ake (Ekisodo 3:1-22; 4:1-9; 5:1-9; 6:1-8; 7:1-7; 14:5-10, 13-31; 15:1-21)
-
11:45 Yehova Ndi Chitsanzo Chabwino Kwambiri pa Nkhani ya Kupirira (Aroma 9:22, 23; 15:13; Yakobo 1:2-4)
-
12:15 Nyimbo Na. 35 ndi Kupuma
MASANA
-
1:25 Kuonera Vidiyo ya Nyimbo
-
1:35 Nyimbo Na. 135
-
1:40 NKHANI YOSIYIRANA: Tizikhalabe Okhulupirika . . .
-
Ena Akamatichitira Zopanda Chilungamo (Mateyu 5:38, 39)
-
Ngati Tikuvutika Chifukwa cha Ukalamba (Yesaya 46:4; Yuda 20, 21)
-
Ngakhale Kuti Si Ife Angwiro (Aroma 7:21-25)
-
Tikapatsidwa Chilango pa Zimene Tinalakwitsa (Agalatiya 2:11-14; Aheberi 12:5, 6, 10, 11)
-
Ngati Tikudwala Matenda Okhalitsa (Salimo 41:3)
-
Tikaferedwa (Salimo 34:18)
-
Tikamazunzidwa (Chivumbulutso 1:9)
-
-
2:55 Nyimbo Na. 85 ndi Zilengezo
-
3:05 SEWERO: Kumbukirani Mkazi wa Loti—Mbali Yoyamba (Luka 17:28-33)
-
3:35 NKHANI YOSIYIRANA: Zimene Zingatithandize Kuti Tizitha Kupirira
-
Chikhulupiriro (Aheberi 11:1)
-
Makhalidwe Abwino (Afilipi 4:8, 9)
-
Kudziwa Zinthu (Miyambo 2:10, 11)
-
Kudziletsa (Agalatiya 5:22, 23)
-
-
4:15 Tingatani Kuti ‘Tisalephere Ngakhale Pang’ono’? (2 Petulo 1:5-10; Yesaya 40:31; 2 Akorinto 4:7-9, 16)
-
4:50 Nyimbo Na. 152 ndi Pemphero Lomaliza