Pulogalamu ya Msonkhano Wadera wa 2017-2018—Womwe Padzakhale Woyang’anira Dera
Onani nkhani za pamsonkhanowu komanso nthawi imene nkhanizo zidzakambidwe, kuphatikizapo nkhani zitatu zimene adzakambe woyang’anira dera.
Musaleke Kuchita Zabwino
N’chifukwa chiyani kuchita zabwino n’kovuta, nanga n’chiyani chomwe chingatithandize kuti tizichita zabwino?
Muzimvetsera Mwachidwi Kuti Mupeze Mayankho a Mafunso Awa
Mafunso amenewa adzayankhidwa pa msonkhano waderawu.