Kukoma Mtima
Kodi timaona umboni wotani wosonyeza kuti Yehova ndi wokoma mtima?
Aro 3:23, 24; Tit 3:3-6; Ahe 2:9; 1Pe 5:5
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Yon 3:10; 4:11—Yehova anakomera mtima anthu a ku Nineve omwe analapa ndipo anamveranso chisoni ziweto zawo
-
Lu 6:32-36—Yesu anatiphunzitsa kuti tizikomerana mtima potikumbutsa kuti Yehova amakomera mtima anthu onse ngakhalenso osayamika ndiponso oipa
-
Kodi tingasonyeze bwanji kukoma mtima kwa anthu ena?
Miy 19:17; 22:9; Lu 6:35; Aef 4:32
Onaninso Miy 11:17; 31:10, 26; Ahe 13:16
-
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
-
Mko 14:3-9; Yoh 12:3—Yesu anayamikira Mariya mlongo wake wa Lazaro chifukwa chochita zinthu mokoma mtima
-
2Ti 1:16-18—Onesiforo analimbikitsa mtumwi Paulo pa nthawi yomwe anali m’ndende
-