Agogo
Nkhani za m’Baibulo zomwe zingakuthandizeni:
1Mf 15:9-13—Mfumu Asa anachita zinthu molimba mtima kwambiri pochotsa agogo ake aakazi pa udindo wawo, ndipo sanalole kuti chibale chimulepheretse kukhala wokhulupirika kwa Yehova
Miy 13:22—Agogo okhulupirika amapereka chitsanzo chabwino poika Yehova pamalo oyamba
Paulo anayamikira agogo ake a Timoteyo a Loisi, chifukwa cha chikhulupiriro chawo chopanda chinyengo komanso chifukwa chophunzitsa bwino Timoteyo zokhudza Yehova