Mfundo Zanga—Zosangalatsa
Chigawo 8
Mfundo Zanga—Zosangalatsa
Tchulani zosangalatsa zimene mumakonda kwambiri, ndipo fotokozani chifukwa chake mumazikonda.
․․․․․
Tayerekezerani kuti mukufuna kufotokozera mng’ono wanu kuti asamangokhalira zisangalalo. Kodi mungamuuze chiyani?
․․․․․