3-A
Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 1)
Mafumu a mu Ufumu Wakum’mwera wa Mafuko Awiri a Yuda
997 B.C.E.
Rehobowamu: zaka 17
980
Abiya (Abiyamu): zaka zitatu
978
Asa: zaka 41
937
Yehosafati: zaka 25
913
Yehoramu: zaka 8
M’ma 906
Ahaziya: chaka chimodzi
M’ma 905
Mfumukazi Ataliya: zaka 6
898
Yehoasi: zaka 40
858
Amaziya: zaka 29
829
Uziya (Azariya): zaka 52
Mafumu a mu Ufumu Wakumpoto wa Mafuko 10 a Isiraeli
997 B.C.E.
Yerobowamu: zaka 22
M’ma 976
Nadabu: zaka ziwiri
M’ma 975
Basa: zaka 24
M’ma 952
Ela: zaka ziwiri
Zimiri: masiku 7 (cha m’ma 951)
M’ma 947
Omuri ndi Tibini: zaka 4
Omuri (yekha): zaka 8
M’ma 940
Ahabu: zaka 22
M’ma 920
Ahaziya: zaka ziwiri
M’ma 917
Yehoramu: zaka 12
M’ma 905
Yehu: zaka 28
876
Yehoahazi: zaka 14
M’ma 862
Yehoahazi ndi Yehoasi: zaka zitatu
M’ma 859
Yehoasi (yekha): zaka 16
M’ma 844
Yerobowamu Wachiwiri: zaka 41
-
Mayina a Aneneri
-
Yoweli
-
Eliya
-
Elisa
-
Yona
-
Amosi