October 9-15
YOBU 4-5
Nyimbo Na. 121 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Samalani ndi Nkhani Zabodza”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 4:4—Kodi Yobu anapereka chitsanzo chabwino chiti kwa Akhristu masiku ano? (w03 5/15 22 ¶5-6)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 5:1-27 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (2 min.) Gwiritsani ntchito nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 4)
Ulendo Wobwereza: (5 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Musonyezeni mmene angapezere zinthu zosiyanasiyana pa jw.org. (th phunziro 15)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 16 mfundo 5 (th phunziro 16)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 60
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 38 ndi Pemphero