October 16-22
YOBU 6-7
Nyimbo Na. 33 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Moyo Ukafika Povuta”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
Yob 6:29—N’chiyani chingatithandize kuti tipewe kuweruza molakwika abale athu? (w20.04 16 ¶10)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) Yob 6:1-21 (th phunziro 2)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 7)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Yambani ndi nkhani imene ili mu chitsanzo cha ulendo wobwereza. Mugawireni chimodzi mwa Zinthu Zophunzitsira. (th phunziro 11)
Nkhani: (5 min.) w22.01 12-13 ¶15-18—Mutu: Tiziphunzitsa Mogwira Mtima Ngati Yakobo —Tizigwiritsa Ntchito Mafanizo Ogwira Mtima. (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova Amapulumutsa Anthu Odzimvera Chisoni”: (15 min.) Nkhani yokambirana komanso vidiyo.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff kubwereza gawo 4
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 143 ndi Pemphero