September 12-18
1 MAFUMU 11-12
Nyimbo Na. 137 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (1 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Sankhani Mwanzeru Munthu Wokwatirana Naye”: (10 min.)
Mfundo Zothandiza: (10 min.)
1Mf 12:21-24—Kodi tikuphunzira chiyani kwa Mfumu Rehobowamu pa nkhani ya kumvera? (w18.06 14 ¶1-4)
Pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno, kodi mwapeza mfundo ziti zokhudza Yehova, utumiki kapena zinthu zina?
Kuwerenga Baibulo: (4 min.) 1Mf 12:21-33 (th phunziro 10)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha zimene tinganene pa ntchito yapadera yoyambitsa maphunziro a Baibulo. (th phunziro 3)
Ulendo Wobwereza: (4 min.) Pitirizani phunziro la Baibulo lomwe munayambitsa pa ulendo woyamba, pogwiritsa ntchito phunziro 01 la kabuku kakuti Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale. (th phunziro 11)
Phunziro la Baibulo: (5 min.) lff phunziro 07 mfundo 4 (th phunziro 8)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Banja Ndi Mgwirizano wa Moyo Wonse”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Kukonzekera Kulowa M’banja—Gawo 3: “Kuwerengera Ndalama Zimene Mudzawononge.”
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) lff phunziro 19 mfundo 1-4
Mawu Omaliza (3 min.)
Nyimbo Na. 63 ndi Pemphero