September 25–October 1
DANIELI 4-6
Nyimbo Na. 67 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Mupitiriza kutumikira Yehova Mosalekeza?”: (10 min.)
Dan. 6:7-10—Danieli anaika moyo wake pangozi n’cholinga choti atumikire Yehova mosalekeza (w10 11/15 6 ¶16; w06 11/1 24 ¶12)
Dan. 6:16, 20—Mfumu Dariyo inazindikira kuti Danieli anali pa ubwenzi wolimba ndi Yehova (w03 9/15 15 ¶2)
Dan. 6:22, 23—Yehova anadalitsa Danieli chifukwa chomulambira molimba mtima (w10 2/15 18 ¶15)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Dan. 4:10, 11, 20-22—Kodi mtengo waukulu womwe Nebukadinezara analota unkaimira chiyani? (w07 9/1 18 ¶5)
Dan. 5:17, 29—N’chifukwa chiyani poyamba Danieli anakana mphatso kuchokera kwa mfumu Belisazara koma pambuyo pake n’kulandira? (w88 10/1 30 ¶3-5; dp 109 ¶22)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Dan. 4:29-37
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) inv
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) inv—Sonyezani mmene mungapangire ulendo wobwereza pogwiritsa ntchito kapepala koitanira anthu kumisonkhano kamene munagawira pa ulendo woyamba.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 120 ¶16—Limbikitsani wophunzira kuti azikhalabe wokhulupirika ngakhale pamene achibale ake akumutsutsa.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Muziwaphunzitsa Kuti Azitumikira Yehova Mosalekeza”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Kenako onetsani ndiponso kukambirana vidiyo imene ikusonyeza wofalitsa waluso ali mu utumiki ndi wofalitsa watsopano.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 7 ¶10-18, komanso tsamba 73
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 73 ndi Pempher