Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

N’chifukwa Chiyani Kuonera Zolaula N’koipa?

N’chifukwa Chiyani Kuonera Zolaula N’koipa?

Masiku ano zolaula zili paliponse ndipo zimapezeka mosavuta. Anthu ambiri, ngakhalenso anthu opemphera, amaona kuti kuonera zolaula kulibe vuto lililonse.

ONERANI VIDIYO YAKUTI KODI KUONERA ZOLAULA NDI TCHIMO?, KENAKO YANKHANI FUNSO LOTSATIRALI:

Kodi malemba otsatirawa angatithandize bwanji kumvetsa mmene Mulungu amamvera pa nkhani yoonera zolaula?