November 18-24
CHIVUMBULUTSO 1-3
Nyimbo Na. 15 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Ndikudziwa Ntchito Zako”: (10 min.)
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Chivumbulutso.]
Chiv. 1:20—Yesu amaona zonse zimene akulu amachita mumpingo (w12 10/15 14 ¶8)
Chiv. 2:1, 2—Yesu amadziwa zimene zimachitika mumpingo uliwonse (w12 4/15 29 ¶11; w01 1/15 20-21 ¶20)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Chiv. 1:7—Kodi diso lililonse lidzamuona bwanji Yesu “akubwera ndi mitambo,” nanga zimenezi zidzachitika liti? (kr 226 ¶10)
Chiv. 2:7—Kodi “kudya za mumtengo wa moyo, umene uli m’paradaiso wa Mulungu,” kumatanthauza chiyani? (w09 1/15 31 ¶1)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Chiv. 1:1-11 (th phunziro 5)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Wobwereza Woyamba: (5 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. (th phunziro 2)
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 5 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba. Yerekezerani kumuonetsa vidiyo yakuti, N’chifukwa Chiyani Tiyenera Kuphunzira Baibulo? kenako kambiranani naye mfundo za m’vidiyoyi. (th phunziro 3)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Yehova Amadziwa Zimene Timafunikira”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onerani vidiyo yakuti Lipoti la Komiti Yophunzitsa la 2017.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 60
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 23 ndi Pemphero