November 11-17
2 YOHANE 1-13; 3 YOHANE 1-14–YUDA 1-25
Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Tiyenera Kuchita Khama Kuti Tikhalebe m’Choonadi”: (10 min.)
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 2 Yohane.]
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la 3 Yohane.]
[Onerani vidiyo ya Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Yuda.]
Yuda 3—Tiyenera “kumenya mwamphamvu nkhondo yachikhulupiriro” (w04 9/15 11-12 ¶8-9)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yuda 4, 12—N’chifukwa chiyani anthu osaopa Mulungu omwe analowa mozemba mumpingo anayerekezeredwa ndi ‘miyala ikuluikulu yobisika m’madzi pa maphwando osonyezana chikondi’? (it-2 279, 816)
Yuda 14, 15—N’chifukwa chiyani Inoki analankhula zam’tsogolo ngati kuti zachitika kale, nanga ulosi wakewu unakwaniritsidwa bwanji? (wp17.1 12 ¶1, 3)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) 2 Yoh. 1-13 (th phunziro 12)
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. (th phunziro 1)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo woyamba. Sonyezani mmene mungayankhire munthu amene wanena zinthu zina zomwe anthu amakonda kunena ngati sakufuna kuti tikambirane nawo. (th phunziro 6)
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Yambani ndi chitsanzo cha ulendo woyamba. Kenako musiyireni khadi lodziwitsa anthu za jw.org. (th phunziro 11)
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 59
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 51 ndi Pemphero