November 5-11
YOHANE 20-21
Nyimbo Na. 35 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Kodi Umandikonda Ine Kuposa Izi?”: (10 min.)
Yoh. 21:1-3—Yesu atangophedwa, Petulo ndi ophunzira ena anapita kukapha nsomba
Yoh. 21:4-14—Yesu ataukitsidwa, anaonekera kwa Petulo komanso ophunzira ena
Yoh. 21:15-19—Yesu anathandiza Petulo kudziwa zinthu zimene ankayenera kuziika patsogolo m’moyo wake (“Yesu anafunsa Simoni Petulo kuti” “kodi umandikonda ine kuposa izi?” “kachitatu” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 21:15, 17, nwtsty)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Yoh. 20:17—Kodi mawu omwe Yesu anauza Mariya Mmagadala akutanthauza chiyani? (“Usandikangamire” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh 20:17, nwtsty)
Yoh. 20:28—N’chifukwa chiyani Tomasi anatchula Yesu kuti “Mbuyanga ndi Mulungu wanga!” (“Mbuyanga ndi Mulungu wanga!” mfundo zimene ndikuphunzira pa Yoh. 20:28, nwtsty)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Yoh. 20:1-18
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Vidiyo ya Ulendo Woyamba: (4 min.) Onerani ndi kukambirana mfundo za m’vidiyoyi.
Ulendo Wobwereza Woyamba: (Osapitirira 3 min.) Gwiritsani ntchito chitsanzo cha ulendo wobwereza woyamba.
Phunziro la Baibulo: (Osapitirira 6 min.) bhs 79 ¶21-22. Kenako muitanireni kumisonkhano yathu.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Zofunika Pampingo: (15 min.)
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 12
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 52 ndi Pemphero