November 6-12
AMOSI 1-9
Nyimbo Na. 144 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Yesetsani Kufunafuna Yehova Kuti Mupitirize Kukhala ndi Moyo”: (10 min.)
[Onetsani vidiyo yakuti Mfundo Zothandiza Kumvetsa Buku la Amosi.]
Amosi 5:4, 6—Tiyenera kudziwa Yehova komanso kumachita zimene amafuna (w04 11/15 24 ¶20)
Amosi 5:14, 15—Tizikonda komanso kutsatira mfundo za Yehova pa nkhani ya zinthu zabwino ndi zoipa (jd 90-91 ¶16-17)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Amosi 2:12—Kodi tingagwiritse ntchito bwanji mfundo zimene tikuphunzira muvesili? (w07 10/1 14 ¶8)
Amosi 8:1, 2—Kodi “dengu la zipatso za m’chilimwe” linkasonyeza chiyani? (w07 10/1 14 ¶6)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Amosi 4:1-13
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Kukonzekera Ulaliki wa Mwezi Uno: (15 min.) Kukambirana “Zitsanzo za Ulaliki.” Pambuyo poonetsa vidiyo ya chitsanzo cha ulaliki iliyonse, kambiranani mfundo zikuluzikulu za m’vidiyoyo.
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
“Kuwonjezera Luso Lathu mu Utumiki—Kupanga Ulendo Wobwereza”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Kenako, onetsani vidiyo yosonyeza ofalitsa awiri akupanga ulendo wobwereza.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 9 ¶16-21 komanso tsamba 94 ndi 95
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 128 ndi Pemphero