Makolo akuphunzitsa ana awo ku South Africa

NDANDANDA YA UTUMIKI KOMANSO MOYO WATHU WACHIKHRISTU June 2018

Zimene Tinganene

Zimene tinganene zokhudza maulosi a m’Baibulo ndi masiku otsiriza.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Yesu Anakwaniritsa Maulosi

Gwirizanitsani zimene zinachitika pa moyo wa Yesu ndi ulosi umene unaneneratu zochitikazo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzitsatira Mapazi a Khristu Mosamala Kwambiri

Yesu ndi chitsanzo chabwino kwambiri chomwe tingatengere makamaka tikamakumana ndi mavuto kapena tikamazunzidwa.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitsanzira Mariya Pokhala Odzichepetsa

Yehova anapatsa Mariya udindo wapadera kwambiri chifukwa anali ndi mtima wabwino.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Ananu, Kodi Mukuyesetsa Kuti Yehova Akhale Mnzanu Wapamtima?

Yesu anasonyeza chitsanzo chabwino kwambiri pa nkhani yokonda Yehova komanso kumvera makolo.

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Makolo, Muzithandiza Ana Anu Kuti Azikonda Kwambiri Yehova

Makolo angathandize ana awo kuti akhale atumiki okhulupirika a Mulungu ngati angachite zilizonse zomwe angathe pophunzitsa anawo mfundo za m’Mawu a Mulungu.

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU

Muzitsanzira Yesu Pokana Mayesero

Kodi Yesu anagwiritsa ntchito chiyani pokana mayesero atatu amene Satana amagwiritsa ntchito kawirikawiri?

MOYO WATHU WACHIKHRISTU

Muzisamala Mukamacheza ndi Anzanu pa Intaneti

Monga mmene zilili ndi zipangizo zambiri zomwe zingakuthandizeni kapena kukuvulazani, malo ochezera a pa intaneti angakhale abwino kapena oipa. Tingathe kugwiritsa ntchito mfundo za m’Baibulo kuti tisiyanitse zoyenera ndi zosayenera.