Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | GENESIS 1-2

Yehova Analenga Zamoyo Padziko Lapansi

Yehova Analenga Zamoyo Padziko Lapansi

1:3, 4, 6, 9, 11, 14, 20, 24, 27

Lembani mwachidule zimene Yehova analenga pamasiku 6 olenga zinthu.

  • Tsiku Loyamba

  • Tsiku Lachiwiri

  • Tsiku Lachitatu

  • Tsiku la 4

  • Tsiku la 5

  • Tsiku la 6