Zimene Tinganene
●○ ULENDO WOYAMBA
Funso: Kodi tingapeze kuti malangizo otithandiza kukhala ndi moyo wosangalala?
Lemba: Sl 1:1, 2
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi kukonda ndalama komanso chuma kungathandize munthu kuti akhale ndi moyo wosangalala?
○● ULENDO WOBWEREZA
Funso: Kodi kukonda ndalama komanso chuma kungathandize munthu kuti akhale ndi moyo wosangalala?
Lemba: 1Ti 6:9, 10
Funso la Ulendo Wotsatira: Kodi kuona zinthu moyenera n’kothandiza bwanji?