Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU | EKISODO 15-16

Tamandani Yehova Poimba Nyimbo

Tamandani Yehova Poimba Nyimbo

15:1, 2, 11, 18, 20, 21

Nyimbo zikhoza kukhudza kwambiri mmene timaganizira komanso mmene timamvera. Kuimba ndi kofunika kwambiri polambira Yehova.

  • Mose ndi Aisiraeli anaimba nyimbo zotamanda Yehova pamene anawapulumutsa mozizwitsa pa Nyanja Yofiira

  • Mfumu Davide anasankha amuna 4,000 kuti akhale oimba pa kachisi

  • Usiku woti afa mawa lake, Yesu ndi ophunzira ake anaimba nyimbo zotamanda Yehova

Kodi ndi pa zochitika ziti pamene ndingakhale ndi mwayi woimba nyimbo zotamanda Yehova?