August 21-27
EZEKIELI 35-38
Nyimbo Na. 132 ndi Pemphero
Mawu Oyamba (Osapitirira 3 min.)
CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Gogi wa ku Magogi Awonongedwa Posachedwapa”: (10 min.)
Ezek. 38:2—Dzina loti Gogi wa ku Magogi likuimira mgwirizano wa mitundu ya anthu (w15 5/15 29-30)
Ezek. 38:14-16—Gogi wa ku Magogi adzaukira atumiki a Yehova (w12 9/15 5-6 ¶8-9)
Ezek. 38:21-23—Yehova Mulungu adzazilemekeza komanso kudziyeretsa powononga Gogi wa ku Magogi (w14 11/15 27 ¶16)
Kufufuza Mfundo Zothandiza: (8 min.)
Ezek. 36:20, 21—Kodi chifukwa chachikulu chimene timafunikira kukhala ndi makhalidwe abwino ndi chiti? (w02 6/15 20 ¶12)
Ezek. 36:33-36—Kodi mawu a mu vesili akukwaniritsidwa bwanji masiku ano? (w88 9/15 24 ¶11)
Kodi mwaphunzira zotani zokhudza Yehova pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kodi ndi mfundo zina ziti zothandiza zimene mwapeza pa kuwerenga Baibulo kwa mlungu uno?
Kuwerenga Baibulo: (Osapitirira 4 min.) Ezek. 35:1-15
KUPHUNZITSA MWALUSO MU UTUMIKI
Ulendo Woyamba: (Osapitirira 2 min.) Sal. 37:29—Kuphunzitsa Choonadi.
Ulendo Wobwereza: (Osapitirira 4 min.) Gen. 1:28; Yes. 55:11—Kuphunzitsa Choonadi.
Nkhani: (Osapitirira 6 min.) w16.07 31-32—Mutu: Kodi Zimene Ezekieli Anauzidwa Kuti Aphatikize Ndodo Ziwiri N’kukhala Imodzi Zikuimira Chiyani?
MOYO WATHU WACHIKHRISTU
Nyimbo Na. 54
“Muzikhala ndi Makhalidwe Amene Mulungu Amasangalala Nawo—Chikhulupiriro”: (15 min.) Nkhani yokambirana. Onetsani vidiyo yakuti Muzichita Zinthu Zimene Zingakulimbikitseni Kukhala Okhulupirika—Chikhulupiriro.
Phunziro la Baibulo la Mpingo: (30 min.) kr mutu 5 ¶18-25 komanso tsamba 57
Mfundo Zimene Taphunzira Komanso za Mlungu Wamawa (3 min.)
Nyimbo Na. 119 ndi Pemphero