A6-B
Tchati: Aneneri Komanso Mafumu a Yuda ndi Isiraeli (Gawo 2)
Mafumu a mu Ufumu Wakumʼmwera (Kupitiriza)
777 B.C.E.
Yotamu: zaka 16
762
Ahazi: zaka 16
746
Hezekiya: zaka 29
716
Manase: zaka 55
661
Amoni: zaka ziwiri
659
Yosiya: zaka 31
628
Yehoahazi: miyezi itatu
Yehoyakimu: zaka 11
618
Yehoyakini: miyezi itatu ndi masiku 10
617
Zedekiya: zaka 11
607
Magulu ankhondo a ku Babulo anawononga Yerusalemu ndi kachisi wake motsogoleredwa ndi Nebukadinezara. Zedekiya, mfumu yomaliza yochokera mumzere wa Davide, inachotsedwa pampando
Mafumu a mu Ufumu Wakumpoto (Kupitiriza)
c. 803 B.C.E.
Zekariya: analamulira kwa miyezi 6 yokha
Tinganene kuti Zekariya anayamba kulamulira, koma zinali zisanatsimikizirike kuti ufumuwo ndi wake mpaka cha mʼma 792
c. 791
Salumu: mwezi umodzi
Menahemu: zaka 10
c. 780
Pekahiya: zaka ziwiri
c. 778
Peka: zaka 20
c. 758
Hoshiya: zaka 9 kuchokera cha mʼma 748
c. 748
Zikuoneka kuti ufumu wa Hoshiya unakhazikika kapena nʼkutheka kuti ankathandizidwa ndi mfumu ya Asuri dzina lake Tigilati-pilesere Wachitatu cha mʼma 748
740
Asuri analanda Samariya, nʼkuyamba kulamulira Aisiraeli; ufumu wa mafuko 10 wa Isiraeli unatha
-
Mayina a Aneneri
-
Yesaya
-
Mika
-
Zefaniya
-
Yeremiya
-
Nahumu
-
Habakuku
-
Danieli
-
Ezekieli
-
Obadiya
-
Hoseya