DISPLAY Buku la M'Baibulo Genesis Ekisodo Levitiko Numeri Deuteronomo Yoswa Oweruza Rute 1 Samueli 2 Samueli 1 Mafumu 2 Mafumu 1 Mbiri 2 Mbiri Ezara Nehemiya Esitere Yobu Masalimo Miyambo Mlaliki Nyimbo ya Solomo Yesaya Yeremiya Maliro Ezekieli Danieli Hoseya Yoweli Amosi Obadiya Yona Mika Nahumu Habakuku Zefaniya Hagai Zekariya Malaki Mateyu Maliko Luka Yohane Machitidwe Aroma 1 Akorinto 2 Akorinto Agalatiya Aefeso Afilipi Akolose 1 Atesalonika 2 Atesalonika 1 Timoteyo 2 Timoteyo Tito Filimoni Aheberi Yakobo 1 Petulo 2 Petulo 1 Yohane 2 Yohane 3 Yohane Yuda Chivumbulutso Chaputala 1 2 3 4 5 6 Kalata Yopita kwa Aefeso Machaputala 1 2 3 4 5 6 Mitu 1 Moni (1, 2) Madalitso auzimu (3-7) Kusonkhanitsa zinthu zonse kwa Akhristu (8-14) Kukhazikitsa “dongosolo” pa nthawi imene anaikiratu (10) Anaikidwa chidindo ndi mzimu woyera ngati “chikole chotsimikizira” (13, 14) Paulo anathokoza Mulungu chifukwa cha chikhulupiriro cha Aefeso ndipo anawapempherera (15-23) 2 Anapangitsa kuti akhale amoyo mogwirizana ndi Khristu (1-10) Anagwetsa khoma lomwe linkawalekanitsa (11-22) 3 Chinsinsi chopatulika chinaphatikizapo anthu a mitundu ina (1-13) Anthu a mitundu ina adzalamulira limodzi ndi Khristu (6) Cholinga chamuyaya cha Mulungu (11) Anapempherera Aefeso kuti akhale ozindikira (14-21) 4 Ogwirizana mʼthupi la Khristu (1-16) Mphatso za amuna (8) Umunthu wakale komanso watsopano (17-32) 5 Malankhulidwe komanso khalidwe loyera (1-5) Muziyenda ngati ana a kuwala (6-14) Mudzazidwe ndi mzimu (15-20) Muzigwiritsa ntchito bwino nthawi yanu (16) Malangizo opita kwa amuna ndi akazi apabanja (21-33) 6 Malangizo opita kwa makolo ndi ana (1-4) Malangizo opita kwa akapolo ndi ambuye (5-9) Zida zonse zankhondo zochokera kwa Mulungu (10-20) Moni womaliza (21-24) Yam'mbuyo Yotsatira Sindikizani Patsani ena Patsani ena Aefeso—Zimene Zili Mʼbukuli BAIBULO LA DZIKO LATSOPANO LA MALEMBA OPATULIKA (LOKONZEDWANSO MU3 2023) Aefeso—Zimene Zili Mʼbukuli Chichewa Aefeso—Zimene Zili Mʼbukuli https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/1001061100/univ/wpub/1001061100_univ_sqr_xl.jpg nwt Ephesians p. 1977