Pitani ku nkhani yake # link, for screen reader ##

Pitani ku mitu ya nkhani

Buku la 2 Mbiri

Machaputala

Mitu

  • 1

    • Solomo anapempha nzeru (1-12)

    • Chuma cha Solomo (13-17)

  • 2

    • Kukonzekera kumanga kachisi (1-18)

  • 3

    • Solomo anayamba kumanga kachisi (1-7)

    • Malo Oyera Koposa (8-14)

    • Zipilala ziwiri zakopa (15-17)

  • 4

    • Guwa lansembe, thanki yosungira madzi ndi mabeseni (1-6)

    • Zoikapo nyale, matebulo ndi mabwalo (7-11a)

    • Kumaliza ntchito yomanga kachisi (11b-22)

  • 5

    • Kukonzekera kutsegulira kachisi  (1-14)

      • Kubweretsa likasa kukachisi (2-10)

  • 6

    • Solomo analankhula ndi anthu (1-11)

    • Pemphero la Solomo lotsegulira kachisi (12-42)

  • 7

    • Kachisi anadzazidwa ndi ulemerero wa Yehova (1-3)

    • Zikondwerero zotsegulira kachisi (4-10)

    • Yehova anaonekera kwa Solomo (11-22)

  • 8

    • Zinthu zina zimene Solomo anamanga (1-11)

    • Anakonza dongosolo lolambirira pakachisi (12-16)

    • Zombo za Solomo (17, 18)

  • 9

    • Mfumukazi ya ku Sheba inapita kwa Solomo (1-12)

    • Chuma cha Solomo (13-28)

    • Imfa ya Solomo (29-31)

  • 10

    • Aisiraeli anagalukira Rehobowamu (1-19)

  • 11

    • Ulamuliro wa Rehobowamu (1-12)

    • Alevi okhulupirika anasamukira ku Yuda (13-17)

    • Banja la Rehobowamu (18-23)

  • 12

    • Sisaki anaukira Yerusalemu (1-12)

    • Kutha kwa ulamuliro wa Rehobowamu (13-16)

  • 13

    • Abiya, mfumu ya Yuda (1-22)

      • Abiya anagonjetsa Yerobowamu (3-20)

  • 14

    • Imfa ya Abiya (1)

    • Asa, mfumu ya Yuda (2-8)

    • Asa anagonjetsa Aitiyopiya 1 miliyoni (9-15)

  • 15

    • Zinthu zimene Asa anasintha (1-19)

  • 16

    • Mgwirizano wa Asa ndi Siriya (1-6)

    • Haneni anadzudzula Asa (7-10)

    • Imfa ya Asa (11-14)

  • 17

    • Yehosafati, mfumu ya Yuda (1-6)

    • Ntchito yophunzitsa anthu (7-9)

    • Asilikali amphamvu a Yehosafati (10-19)

  • 18

    • Mgwirizano wa Yehosafati ndi Ahabu (1-11)

    • Mikaya analosera zoti agonjetsedwa (12-27)

    • Ahabu anaphedwa ku Ramoti-giliyadi (28-34)

  • 19

    • Yehu anadzudzula Yehosafati (1-3)

    • Zinthu zimene Yehosafati anasintha (4-11)

  • 20

    • Mayiko ozungulira anayamba kuopseza Ayuda (1-4)

    • Yehosafati anapempha Mulungu kuti amuthandize (5-13)

    • Mmene Yehova anamuyankhira (14-19)

    • Ayuda anapulumutsidwa modabwitsa (20-30)

    • Kutha kwa ulamuliro wa Yehosafati (31-37)

  • 21

    • Yehoramu, mfumu ya Yuda (1-11)

    • Uthenga umene Eliya analemba (12-15)

    • Mapeto omvetsa chisoni a Yehoramu (16-20)

  • 22

    • Ahaziya, mfumu ya Yuda (1-9)

    • Ataliya analanda ufumu (10-12)

  • 23

    • Yehoyada anathandiza kuti Yehoasi akhale mfumu (1-11)

    • Ataliya anaphedwa (12-15)

    • Zinthu zomwe Yehoyada anasintha (16-21)

  • 24

    • Ulamuliro wa Yehoasi (1-3)

    • Yehoasi anakonza kachisi (4-14)

    • Yehoasi anayamba kulambira mafano (15-22)

    • Yehoasi anaphedwa (23-27)

  • 25

    • Amaziya, mfumu ya Yuda (1-4)

    • Anamenyana ndi Aedomu (5-13)

    • Amaziya anayamba kulambira mafano (14-16)

    • Anamenyana ndi Yehoasi mfumu ya Isiraeli (17-24)

    • Imfa ya Amaziya (25-28)

  • 26

    • Uziya, mfumu ya Yuda (1-5)

    • Nkhondo zimene Uziya anamenya (6-15)

    • Uziya anachititsidwa khate chifukwa chodzikuza (16-21)

    • Imfa ya Uziya (22, 23)

  • 27

    • Yotamu, mfumu ya Yuda (1-9)

  • 28

    • Ahazi, mfumu ya Yuda (1-4)

    • Anagonjetsedwa ndi Siriya komanso Isiraeli (5-8)

    • Odedi anachenjeza Isiraeli (9-15)

    • Ayuda anatsitsidwa (16-19)

    • Ahazi anayamba kulambira mafano; imfa ya Ahazi (20-27)

  • 29

    • Hezekiya, mfumu ya Yuda (1, 2)

    • Zinthu zimene Hezekiya anasintha (3-11)

    • Kuyeretsa kachisi (12-19)

    • Anayambiranso utumiki wapakachisi (20-36)

  • 30

    • Hezekiya anachita Pasika (1-27)

  • 31

    • Hezekiya anathetsa kulambira mafano (1)

    • Ansembe ndi Alevi anayamba kuthandizidwa (2-21)

  • 32

    • Senakeribu anaopseza Yerusalemu (1-8)

    • Senakeribu ananyoza Yehova (9-19)

    • Mngelo anapha asilikali a Asiriya (20-23)

    • Hezekiya anadwala kenako anadzikuza (24-26)

    • Zimene Hezekiya anachita; imfa ya Hezekiya (27-33)

  • 33

    • Manase, mfumu ya Yuda (1-9)

    • Manase analapa machimo ake (10-17)

    • Imfa ya Manase (18-20)

    • Amoni, mfumu ya Yuda (21-25)

  • 34

    • Yosiya, mfumu ya Yuda (1, 2)

    • Zinthu zomwe Yosiya anasintha (3-13)

    • Anapeza buku la Chilamulo (14-21)

    • Hulida analosera za tsoka (22-28)

    • Yosiya anawerengera anthu buku (29-33)

  • 35

    • Yosiya anakonza zoti achite pasika (1-19)

    • Yosiya anaphedwa ndi Farao Neko (20-27)

  • 36

    • Yehoahazi, mfumu ya Yuda (1-3)

    • Yehoyakimu, mfumu ya Yuda (4-8)

    • Yehoyakini, mfumu ya Yuda (9, 10)

    • Zedekiya, mfumu ya Yuda (11-14)

    • Yerusalemu anawonongedwa (15-21)

    • Koresi analamula kuti kachisi amangidwenso (22, 23)