Kukaona Malo pa Beteli
Tikuitanani kuti mudzaone maofesi athu a nthambi, amene timayacha kuti Beteli. Maofesi ena a nthambi ali na ma miziyamu yakuti munthu akhoza kudzionela yekha zinthu popanda wina kumutsogolela.
South Africa
1 Robert Broom Drive East
Rangeview
KRUGERSDORP
1739
SOUTH AFRICA
+27 11-761-1000
Kuona Malo
Pa Mande mpaka pa Cisanu
7:45hrs mpaka 11:00hrs ndi 13:00hrs mpaka 16:00hrs.
Nthawi yoona malo: Maola aŵili
Zimene Timacita
Timasindikiza mabuku, magazini, tumabuku ndi tumapepala twa uthenga m’zinenelo 121 ndi kutumiza ku mipingo yoposa 12,000 m’maiko 11. Timamasulila mabuku m’zinenelo 20. Timathandizanso pa nchito yomanga Nyumba za Ufumu m’maiko 42.