December 17-23
MACHITIDWE 15-16
Nyimbo 96 na Pemphelo
Mawu Oyamba (3 min. olo kucepelapo)
CUMA COPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
“Cigamulo Cozikidwa pa Mawu a Mulungu”: (10 min.)
Mac. 15:1, 2—Nkhani ya mdulidwe inakula moti ikanagaŵanitsa mpingo woyambilila wacikhristu (bt mapeji 102-103 pala. 8)
Mac. 15:13-20—Cigamulo ca bungwe lolamulila cinali cozikidwa pa Malemba (w12 1/15 peji 5 mapa. 6-7)
Mac. 15:28, 29; 16:4, 5—Cigamulo ca bungwe lolamulila cinalimbitsa mipingo (bt peji 123 pala. 18)
Kufufuza Cuma ca Kuuzimu: (8 min.)
Mac. 16:6-9—Kodi nkhaniyi itiphunzitsa ciani za kuwonjezela utumiki wathu? (w12 1/15 peji 10 pala. 8)
Mac. 16:37—Kodi mtumwi Paulo anaseŵenzetsa bwanji unzika wake waciroma kuti akwanilitse nchito yolalikila uthenga wabwino? (““ndife Aroma” nwtsty mfundo younikila)
Kodi imwe pacanu, kuŵelenga Baibo kwa wiki ino kwakuphunzitsani ciani za Yehova?
Ni cuma ca kuuzimu cina citi cimene mwapeza pa kuŵelenga Baibo kwa wiki ino?
Kuŵelenga Baibo: (4 min. olo kucepelapo) Mac. 16:25-40
CITANI KHAMA PA ULALIKI
Ulendo Woyamba: (2 min. olo kucepelapo) Yambani na makambilano acitsanzo. Yankhani pa zimene anthu a m’gawo lanu amakamba posafuna kuwalalikila.
Kubwelelako Koyamba: (3 min. olo kucepelapo) Seŵenzetsani makambilano acitsanzo. Chulani na kukambilana vidiyo yakuti N’cifukwa Ciani Muyenela Kuphunzila Baibulo? (koma musaitambitse)
Vidiyo ya Kubwelelako Kaciŵili: (5 min.) Tambitsani na kukambilana vidiyoyi.
UMOYO WATHU WACIKHRISTU
“Muziimba Mosangalala Nyimbo Zotamanda Yehova”: (15 min.) Kukambilana. Tambitsani vidiyo yakuti Ana Atamanda Yehova m’Nyimbo. Potsiliza mbaliyi, pemphani onse kuti aimilile na kuimbila pamodzi nyimbo ya pa vidiyo, namba 084 ya mutu wakuti Kudzipeleka na Mtima Wonse.
Phunzilo la Baibo la Mpingo: (30 min.) jy mutu 46
Kubwelelamo na Kuchulako za Wiki Yotsatila (3 min.)
Nyimbo 102 na Pemphelo