Nyimbo Nambala 53—Tigwire Ntchito Mogwirizana
Imbani nawo nyimboyi kuti mudziwe mmene anthu a Yehova alili ogwirizana padziko lonse.
Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi
ZOCHITA PA GAWO LA KHALANI BWENZI LA YEHOVA
Kodi Zithunzizi Zikusiyana Pati?: Zochita Zokhudza Misonkhano
Yerekezerani zithunzizi. Kodi chingakuthandizeni ndi chiyani kuti muzimvetsera kwambiri nthawi ya misonkhano?
MAVIDIYO
Phunzirani kwa Anzake a Yehova
Phunzirani zambiri kuchokera kwa anthu otchulidwa m’Baibulo omwe anakhala mabwenzi a Yehova!
ZIMENE BAIBULO LIMAPHUNZITSA
Zoti Ana Achite
Gwiritsani ntchito zinthu zosangalatsa zimenezi, nkhani zochokera m’Baibulo komanso makadi a anthu otchulidwa m’Baibulo pophunzitsa ana mfundo za m’Baibulo.