KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Debora

Debora

Pulintani zochitazi kuti muphunzire kwa Debora yemwe anali mnzake wa Yehova.

Makolo werengani ndi kukambirana limodzi ndi ana anu Oweruza 4:4-10.

Pangani dawunilodi komanso kupulintani zochita.

Dulani zithunzi zimene zili patsamba loyamba ndipo muzitsatira malangizo pamene mukuzimata pamalo oyenerera patsamba lachiwiri. Pezerani limodzi mayankho a mafunso a muvidiyo. Ngati mulinso ndi tizithunzi tina tomwe munadula m’mbuyomu, mukhoza kutimata pamodzi n’kupanga kabuku.