Yehova Mulungu Adzakuthandizani

Yehova Mulungu Adzakuthandizani

Vidiyoyi ikusonyeza mmene lemba limodzi la m’Baibulo lathandizira Grayson kudziwa kuti sizichita kufunika kuti munthu akhale wangwiro kuti athe kuchita zinthu zosangalatsa Mulungu.